“Koma pali yemwe wawinako?” – Ambiri anyinyirika ndi mpikisano wa Coca-cola
Pomwe mpikisano uliwonse umayenera kupindulira kampani komaso makasitomala, zikuwoneka kuti mpikisano wa Coca-Cola ukupindulira mbali imodzi yokha pomwe makasitomala ambiri ati akukaikira ngati anthu akupambanadi mphoto.Kampani ya Coca-Cola inakhazikitsa mpikisano mwezi wapitawo, omwe uli mkati pano ndipo ukupereka mpata kwa anthu mwayi opambana mphoto yomwe yalembedwa mkati mwachitsekerero cha botolo la chakumwa chawo.Izi zapangitsa anthu...Coca-Cola·Malawi Gaming and Lotteries Authority (MAGLA