Skip to content
Standard
Reader
Log in
Tag
Ngongole
Articles and publications tagged Ngongole across the Atmosphere.
1
article
1
publication
Articles
Publications
Recent
Recent
Trending
Most popular
Malawi24
·
Sep 28, 2026
Wophunzira afuna kudzipha kaamba ka ngongole
Wophunzira wina pa sukulu yaukachenjede ya University of Malawi (UNIMA) amafuna kuchotsa moyo wake posowa mtendere ndi ngongole ya pafupifupi K600,000 yomwe akukanika kubweza.Joseph Nenani Major, yemwe ali m’chaka chachitatu, wati wakhala akubwereka ndalama kwa anthu angapo kuti adzithandizire pa maphunziro ake.Iye wati chili chonse chokhudza maphunziro ake amadzipangira yekha choncho anabwereka K594,500 kwa anthu...
Debt
·
Ngongole
You've reached the end.
Home
Latest
Discover
Search