Ndinawona lamya zitatu za Chilima — msilikali Chagonapanja
Mafunso a komwe kudapita lamya ina ya malemu Saulos Chilima amanga nthenje tsopano pomwe mboni ya chisilikali yati idawona mafoni atatu osati awiri okha.Lachitatu madzulo, Major General Richard Chagonapanja adawonekera ku komiti yapadera yomwe ikufufuza za ngozi yandege yaku Chikangawa pa 10 June, 2024.Major General Chagonapanja adauza komitiyi kuti iye ndiamene ankatsogolera a silikali a...Major General Richard Chagonapanja·Mary Chilima