Pa ngozi ya ndege zovala zimatha kuvuka — mboni
Pomwe kafukufuku wokhudza ngozi ya ndege akupitirira, mboni ina yati zomwe zinachitika kuti anthu ena okhudzidwa anapezeka alibe zovala zina, sizachilendo.Wapolisi wofufuza Harry Mbewe wawuza komiti ya kafukufuku wa ndege kuti mphamvu ya ngozi ya ndege imatha kuvula komaso kung'amba zovala za anthu okhudzidwa.Iwo mayankhula izi pomwe anafusidwa kuti afotokoze bwino pomwe zithuzi zina zangozi...Harry Mbewe·Plane Crash Inquiry