Mafoni anali osaswekwa — Mitaye
...watsutsa umboni wa Muwanga Pomwe kusaka mayankho pa ngozi ya ndege kukupitirira, usiku wapitawu kwatuluka umboni wina omwe wabweretsaso mafunso. Mboni ina yati inapeza mafoni awiri omwe anali osaswekwa.Izi ndi malingana ndi a Glinton Mitaye omwe anali wachiwiri kwa mkulu wa apolisi mchigawo cha kumpoto omwe anawonekera ku komiti yomwe ikufufuza za ngozi ya ndege...Glinton Mitaye·Mary Chilima