Tikufuna tisiye kuchinyitsa kwambiri – Ekhaya
Pomwe ligi yaikulu ya FDH Premiership ikubwerera m’bwalo lero, matimu achenjezedwa ofuna pagolo pa Ekhaya avale dzilimbe apo bii sapaona.Mphunzitsi wa Ekhaya Fundi Akidu, wati limodzi mwa vuto lomwe timuyi yakumana nalo mchigawo choyamba chapitachi, ndilogoletsetsa zigoli zochuluka.Akidu amalunkhula izi Lachisanu pomwe Ekhaya ikuyembekezeka kuzepulana ndi Kamuzu Barracks lero Loweluka pa bwalo la Mpira ku...Ekhaya·FDH Bank Premiership