NRB iyamba gawo lachinayi la kalembera wa ana
Bungwe la National Registration Bureau (NRB) lati liyamba gawo la chinayi la kalembera wa ana m’maboma anayi.Malingana ndi kalata yachidziwitso yomwe wasayinira ndi mlembi wamkulu wa NRB, Patrick Machika, kalemberayu achitika m'maboma a Mulanje, Thyolo, Chikwawa ndi Nsanje.Bungweli lati kalemberayu adzachitika kuyambira la Chiwiri pa 28 July mpaka la Chinayi pa 6 August 2026.NRB yati...birth certificate·Birth Registration